Yesaya 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye wati: “Usadzakondwerenso+ namwaliwe, mwana wamkazi wa Sidoni+ woponderezedwa. Nyamuka, wolokera ku Kitimu.+ Koma ngakhale kumeneko, sukapezako mpumulo.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:12 Nsanja ya Olonda,10/15/2007, tsa. 17 Yesaya 1, ptsa. 251-252
12 Iye wati: “Usadzakondwerenso+ namwaliwe, mwana wamkazi wa Sidoni+ woponderezedwa. Nyamuka, wolokera ku Kitimu.+ Koma ngakhale kumeneko, sukapezako mpumulo.”