Yesaya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:13 Yesaya 1, ptsa. 280-281
13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+