Yesaya 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:19 Galamukani!,5/8/2004, ptsa. 19-20 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 20 Yesaya 1, tsa. 282
19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+