Yesaya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu n’kukhala wamphamvu ngati mtengo. Isiraeli+ adzakhala ngati mtengo waukulu wa maluwa ambiri. Iwo adzabereka zipatso panthaka ya dziko lonse lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:6 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 227/1/1995, tsa. 21 Yesaya 1, tsa. 286
6 M’masiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu n’kukhala wamphamvu ngati mtengo. Isiraeli+ adzakhala ngati mtengo waukulu wa maluwa ambiri. Iwo adzabereka zipatso panthaka ya dziko lonse lapansi.+