Yesaya 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kwa iwowo mawu a Yehova adzakhaladi “lamulo pa lamulo, lamulo pa lamulo, chingwe choyezera pachingwe choyezera, chingwe choyezera pachingwe choyezera,+ apa pang’ono, apo pang’ono,” kuti akagwe chagada n’kuthyoka, kukodwa ndi kugwidwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:13 Yesaya 1, ptsa. 291-292 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 14-15
13 Kwa iwowo mawu a Yehova adzakhaladi “lamulo pa lamulo, lamulo pa lamulo, chingwe choyezera pachingwe choyezera, chingwe choyezera pachingwe choyezera,+ apa pang’ono, apo pang’ono,” kuti akagwe chagada n’kuthyoka, kukodwa ndi kugwidwa.+