2 Mafumu 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithu ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya,+ ndiponso ndidzamuyeza ndi thabwa lowongolera limene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzam’pukuta+ mpaka kuyera mbee ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera mbee, n’kuitembenuza.+ Yesaya 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chilungamo+ ndidzachisandutsa chingwe choyezera+ ndipo ndidzachisandutsanso chipangizo chowongolera.* Mvula yamatalala+ idzakokolola malo othawirapo abodza + ndipo madzi adzasefukira pamalo obisalako.+ Maliro 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.
13 Ndithu ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya,+ ndiponso ndidzamuyeza ndi thabwa lowongolera limene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzam’pukuta+ mpaka kuyera mbee ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera mbee, n’kuitembenuza.+
17 Chilungamo+ ndidzachisandutsa chingwe choyezera+ ndipo ndidzachisandutsanso chipangizo chowongolera.* Mvula yamatalala+ idzakokolola malo othawirapo abodza + ndipo madzi adzasefukira pamalo obisalako.+
8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.