-
Ezekieli 23:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Udzaledzera kwambiri ndi kudzazidwa ndi chisoni. Udzaledzera ndi zinthu za m’kapu ya mkulu wako Samariya, zinthu zodabwitsa kwambiri ndi zowononga.
-