1 Mafumu 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli. 2 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+
21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.
11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+