Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+

  • Yesaya 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chilungamo+ ndidzachisandutsa chingwe choyezera+ ndipo ndidzachisandutsanso chipangizo chowongolera.* Mvula yamatalala+ idzakokolola malo othawirapo abodza + ndipo madzi adzasefukira pamalo obisalako.+

  • Yesaya 34:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mbalame zotchedwa vuwo ndi nungu zidzakhala kumeneko. Komanso akadzidzi a makutu ataliatali ndi akhwangwala azidzakhala kumeneko.+ Iye adzatambasulira dzikolo chingwe choyezera+ malo opanda kanthu, ndiponso miyala yoyezera kuwongoka kwa chinthu.

  • Maliro 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.

      Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+

      Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena