Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndi kuwayeza ndi chingwe. Iye anawagoneka pansi kuti ayeze zingwe ziwiri ndi kuwapha, ndiponso chingwe chimodzi chathunthu n’kuwasiya amoyo.+ Choncho Amowabu anakhala atumiki a Davide+ ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+

  • 2 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithu ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya,+ ndiponso ndidzamuyeza ndi thabwa lowongolera limene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzam’pukuta+ mpaka kuyera mbee ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera mbee, n’kuitembenuza.+

  • Yesaya 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kwa iwowo mawu a Yehova adzakhaladi “lamulo pa lamulo, lamulo pa lamulo, chingwe choyezera pachingwe choyezera, chingwe choyezera pachingwe choyezera,+ apa pang’ono, apo pang’ono,” kuti akagwe chagada n’kuthyoka, kukodwa ndi kugwidwa.+

  • Maliro 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova waganiza zogwetsa mpanda+ wa mwana wamkazi wa Ziyoni.

      Watambasula chingwe choyezera.+ Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.+

      Walilitsa+ chiunda chomenyerapo nkhondo ndi mpanda. Zonsezi zatha mphamvu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena