Yesaya 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi iye akasalaza dothilo si paja amawazapo chitowe chakuda ndiponso amafesapo chitowe chamtundu wina?+ Kodi si paja amabzalanso tirigu, mapira+ ndi balere m’malo ake,+ ndipo m’mphepete mwa mundawo+ amabzalamo mbewu zinanso?*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:25 Nsanja ya Olonda,10/1/2001, tsa. 11
25 Kodi iye akasalaza dothilo si paja amawazapo chitowe chakuda ndiponso amafesapo chitowe chamtundu wina?+ Kodi si paja amabzalanso tirigu, mapira+ ndi balere m’malo ake,+ ndipo m’mphepete mwa mundawo+ amabzalamo mbewu zinanso?*+