Yesaya 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye akamaliza kusalaza dothiloKodi sawazapo chitowe chakuda ndiponso kufesa chitowe chamtundu wina?Ndipo kodi sadzala tirigu, mapira ndi balere mʼmalo ake,Komanso mbewu zina*+ mʼmphepete mwa mundawo? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:25 Nsanja ya Olonda,10/1/2001, tsa. 11
25 Iye akamaliza kusalaza dothiloKodi sawazapo chitowe chakuda ndiponso kufesa chitowe chamtundu wina?Ndipo kodi sadzala tirigu, mapira ndi balere mʼmalo ake,Komanso mbewu zina*+ mʼmphepete mwa mundawo?