Yesaya 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzalanditsa iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri, ndipo ndidzateteza mzinda uno.+