Yesaya 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine sindinalankhule m’malo obisika,+ m’malo amdima a padziko lapansi. Sindinauze mbewu ya Yakobo kuti, ‘Anthu inu muzindifunafuna pachabe.’+ Ine ndine Yehova, wolankhula zolungama, wonena zowongoka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:19 Yesaya 2, ptsa. 88-90
19 Ine sindinalankhule m’malo obisika,+ m’malo amdima a padziko lapansi. Sindinauze mbewu ya Yakobo kuti, ‘Anthu inu muzindifunafuna pachabe.’+ Ine ndine Yehova, wolankhula zolungama, wonena zowongoka.+