Yesaya 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine sindinalankhule mʼmalo obisika,+ mʼdziko lamdima.Sindinauze mbadwa* za Yakobo kuti,‘Muzindifunafuna pachabe.’ Ine ndine Yehova, amene ndimalankhula zolungama komanso kulengeza zinthu zimene ndi zolondola.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:19 Yesaya 2, ptsa. 88-90
19 Ine sindinalankhule mʼmalo obisika,+ mʼdziko lamdima.Sindinauze mbadwa* za Yakobo kuti,‘Muzindifunafuna pachabe.’ Ine ndine Yehova, amene ndimalankhula zolungama komanso kulengeza zinthu zimene ndi zolondola.+