Yesaya 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ ndi akuti: “Ine ndidzamusonkhanitsiranso anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:8 Yesaya 2, tsa. 257
8 Mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ ndi akuti: “Ine ndidzamusonkhanitsiranso anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+