Yesaya 56:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tabwerani amuna inu! Dikirani kaye ndikatenge vinyo. Timwe mpaka kuledzera.+ Mawa lidzakhalanso ngati lero, mwinanso kuposa pamenepa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:12 Yesaya 2, ptsa. 258-259
12 “Tabwerani amuna inu! Dikirani kaye ndikatenge vinyo. Timwe mpaka kuledzera.+ Mawa lidzakhalanso ngati lero, mwinanso kuposa pamenepa.”+