Yeremiya 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova wanena kuti: “Tsopano nditaya kutali anthu okhala padziko lapansi,+ ndipo ndiwachititsa kuvutika mtima kuti adziwe masautso awo.”+
18 Yehova wanena kuti: “Tsopano nditaya kutali anthu okhala padziko lapansi,+ ndipo ndiwachititsa kuvutika mtima kuti adziwe masautso awo.”+