Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:63
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+

  • 1 Samueli 25:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu+ adzakulunga ndi kuteteza moyo wanu m’phukusi la moyo+ monga mmene munthu amatetezera chuma chake. Koma moyo wa adani anu adzauponya ndi kuutaya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*+

  • Yeremiya 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho ndidzakutayani kunja kukuchotsani m’dziko lino+ ndi kukupititsani kudziko limene inu ngakhalenso makolo anu sanalidziwe.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina+ usana ndi usiku chifukwa sindidzakumverani chifundo.”’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena