Yeremiya 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzikoli ladzaza+ ndi anthu achigololo+ ndipo chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+ ndipo malo a m’chipululu odyetsera ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo mopanda chilungamo.
10 Dzikoli ladzaza+ ndi anthu achigololo+ ndipo chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+ ndipo malo a m’chipululu odyetsera ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo mopanda chilungamo.