Yeremiya 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzikoli ladzaza ndi anthu achigololo.+Chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+Ndipo malo amʼchipululu odyetserako ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo molakwika.
10 Dzikoli ladzaza ndi anthu achigololo.+Chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+Ndipo malo amʼchipululu odyetserako ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo molakwika.