Yeremiya 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngati iwo akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,+ akanachititsa anthu anga kumva mawu anga, ndipo akanabweza anthu anga panjira zawo zoipa komanso pa zochita zawo zoipa.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:22 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 11
22 Ngati iwo akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,+ akanachititsa anthu anga kumva mawu anga, ndipo akanabweza anthu anga panjira zawo zoipa komanso pa zochita zawo zoipa.”+