Yeremiya 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ngati akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,Akanachititsa kuti anthu anga amve mawu angaNdipo akanawachititsa kuti abwerere nʼkusiya kuyenda mʼnjira zawo zoipa komanso kusiya zochita zawo zoipa.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:22 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 11
22 Koma ngati akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,Akanachititsa kuti anthu anga amve mawu angaNdipo akanawachititsa kuti abwerere nʼkusiya kuyenda mʼnjira zawo zoipa komanso kusiya zochita zawo zoipa.”+