Yeremiya 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino,+ ndipo ndidzawabwezeretsa kudziko lino.+ Pamenepo ndidzawalimbitsa, osati kuwapasula. Ndidzawabzala, osati kuwazula.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:6 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 14-15, 171/1/1986, ptsa. 18-19
6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino,+ ndipo ndidzawabwezeretsa kudziko lino.+ Pamenepo ndidzawalimbitsa, osati kuwapasula. Ndidzawabzala, osati kuwazula.+