Yeremiya 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino ndipo ndidzachititsa kuti abwerere mʼdziko lino.+ Ndidzachititsa kuti zinthu ziziwayendera bwino ndipo sindidzawawononga. Ndidzawadzala ndipo sindidzawazula.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:6 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 14-15, 171/1/1986, ptsa. 18-19
6 Maso anga adzakhala pa iwo kuti ndiwachitire zabwino ndipo ndidzachititsa kuti abwerere mʼdziko lino.+ Ndidzachititsa kuti zinthu ziziwayendera bwino ndipo sindidzawawononga. Ndidzawadzala ndipo sindidzawazula.+