-
Yeremiya 34:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Yehova analankhula ndi Yeremiya pamene Nebukadirezara mfumu ya Babulo,+ gulu lake lonse lankhondo,+ maufumu onse a padziko lapansi, maulamuliro amene anali m’manja mwake+ ndiponso pamene mitundu yonse ya anthu inali kumenyana ndi mzinda wa Yerusalemu, ndi mizinda yonse yozungulira mzindawo.+ Iye anati:
-