34 Yehova analankhula ndi Yeremiya pamene Nebukadinezara mfumu ya Babulo, asilikali ake onse, maufumu onse apadziko lapansi amene anali pansi pa ulamuliro wake ndiponso mitundu yonse ya anthu ankamenyana ndi Yerusalemu komanso mizinda yake yonse. Iye anati:+