Yeremiya 44:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kodi Yehova sanakumbukire nsembe zautsi zimene munali kufukiza m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu?+ Kodi nsembe zimene inuyo,+ makolo anu,+ mafumu anu,+ akalonga anu+ ndi anthu a m’dzikolo anali kupereka, sizinalowe mumtima mwake?+
21 “Kodi Yehova sanakumbukire nsembe zautsi zimene munali kufukiza m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu?+ Kodi nsembe zimene inuyo,+ makolo anu,+ mafumu anu,+ akalonga anu+ ndi anthu a m’dzikolo anali kupereka, sizinalowe mumtima mwake?+