Yeremiya 44:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Nsembe zimene inuyo, makolo anu, mafumu anu, akalonga anu ndi anthu amʼdzikolo ankapereka mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu,+ Yehova anazikumbukira ndipo zinalowa mumtima mwake.
21 “Nsembe zimene inuyo, makolo anu, mafumu anu, akalonga anu ndi anthu amʼdzikolo ankapereka mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu,+ Yehova anazikumbukira ndipo zinalowa mumtima mwake.