Yeremiya 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Mowabu wafunkhidwa, ndipo munthu wina adzaukira mizinda yake.+ Anyamata osankhidwa a m’mizindayo apita kokaphedwa,’+ yatero Mfumu imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+
15 “‘Mowabu wafunkhidwa, ndipo munthu wina adzaukira mizinda yake.+ Anyamata osankhidwa a m’mizindayo apita kokaphedwa,’+ yatero Mfumu imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+