Maliro 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akutithamangitsa ndipo atsala pang’ono kutigwira.+ Tatopa ndipo tikusowa mpumulo.+