-
Ezekieli 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndinaona chinachake chowala ngati siliva wosakanikirana ndi golide,+ chooneka ngati kuti mkati mwake monse mukuyaka moto.+ Kuchokera pa chimene chinali kuoneka ngati chiuno chake kupita m’mwamba ndiponso kutsika m’munsi, munthuyo anali kuoneka ngati moto, ndipo pamalo onse omuzungulira panali powala.
-