Ezekieli 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utulutse katundu wako monga katundu wopita naye ku ukapolo. Umutulutse masana iwo akuona. Madzulo, iweyo unyamuke iwo akuona. Unyamuke ngati mmene amachitira anthu otengedwa kupita ku ukapolo.+
4 Utulutse katundu wako monga katundu wopita naye ku ukapolo. Umutulutse masana iwo akuona. Madzulo, iweyo unyamuke iwo akuona. Unyamuke ngati mmene amachitira anthu otengedwa kupita ku ukapolo.+