Ezekieli 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Masana iwo akuona, utulutse katundu wako amene walongedza kuti upite naye ku ukapolo. Ndiyeno madzulo iwo akuona, unyamuke ngati munthu amene watengedwa kupita ku ukapolo.+
4 Masana iwo akuona, utulutse katundu wako amene walongedza kuti upite naye ku ukapolo. Ndiyeno madzulo iwo akuona, unyamuke ngati munthu amene watengedwa kupita ku ukapolo.+