Ezekieli 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mizinda ya anthu idzawonongedwa.+ Dzikolo lidzangokhala bwinja lokhalokha,+ ndipo inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
20 Mizinda ya anthu idzawonongedwa.+ Dzikolo lidzangokhala bwinja lokhalokha,+ ndipo inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+