Yesaya 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu azidzapita kumeneko atanyamula mivi ndi mauta,+ chifukwa m’dziko lonselo mudzamera tchire la zitsamba zaminga ndi udzu. Yeremiya 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinaliona dzikolo, ndipo linali lopanda kanthu ndi lachabechabe.+ Ndinayang’ana kumwamba ndipo sikunali kuwala.+
24 Anthu azidzapita kumeneko atanyamula mivi ndi mauta,+ chifukwa m’dziko lonselo mudzamera tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.
23 Ndinaliona dzikolo, ndipo linali lopanda kanthu ndi lachabechabe.+ Ndinayang’ana kumwamba ndipo sikunali kuwala.+