9 Anthu okhala m’mizinda ya Isiraeli adzakoleza moto pogwiritsa ntchito zida zankhondo. Zida zake ndizo zishango zazing’ono, zishango zazikulu, mauta, mivi, zobayira ndi mikondo ing’onoing’ono. Adzakoleza moto+ pogwiritsa ntchito zida zimenezi kwa zaka 7.