Yoswa 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ pakuti mawa pa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundula,*+ ndipo magaleta awo udzawatentha ndi moto.”+ Salimo 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+
6 Pamenepo Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ pakuti mawa pa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundula,*+ ndipo magaleta awo udzawatentha ndi moto.”+
9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+