Ezekieli 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero iwe uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Sindidzazengerezanso pa zimene ndalankhula.+ Mawu alionse amene ndalankhula adzakwaniritsidwadi,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:28 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
28 Chotero iwe uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Sindidzazengerezanso pa zimene ndalankhula.+ Mawu alionse amene ndalankhula adzakwaniritsidwadi,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”+