Yeremiya 44:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu amene adzathawa lupanga kuchoka ku Iguputo kubwerera kudziko la Yuda adzakhala ochepa.+ Ndipo otsala onse ochokera ku Yuda amene akubwera m’dziko la Iguputo kuti adzakhalemo monga alendo adzadziwa kuti ndi mawu a ndani amene ali oona, mawu anga kapena mawu awo.”’”+ Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+ Chivumbulutso 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+
28 Anthu amene adzathawa lupanga kuchoka ku Iguputo kubwerera kudziko la Yuda adzakhala ochepa.+ Ndipo otsala onse ochokera ku Yuda amene akubwera m’dziko la Iguputo kuti adzakhalemo monga alendo adzadziwa kuti ndi mawu a ndani amene ali oona, mawu anga kapena mawu awo.”’”+
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+