Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, pamene iwo akukhala m’dziko la adani awo, sindidzawakana+ kapena kunyansidwa nawo+ moti n’kuwafafaniziratu, kuphwanya pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo.

  • Yesaya 27:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 M’tsiku limenelo kudzalira lipenga lomveka kutali.+ Ndiyeno anthu amene akuwonongeka m’dziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana m’dziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira+ Yehova m’phiri loyera ku Yerusalemu.+

  • Yeremiya 44:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Sipadzapezeka aliyense wothawa kapena wopulumuka mwa otsala a Yuda amene alowa m’dziko la Iguputo ndi kukhala mmenemo monga alendo,+ kupatulapo anthu ochepa chabe amene adzathawa. Sipadzapezeka wobwerera kudziko la Yuda kumene akulakalaka kubwerera kuti akakhaleko.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena