Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Zekariya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+
16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+