1 Samueli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chaka ndi chaka+ iye anali kuchita zimenezi nthawi zonse akapita kunyumba ya Yehova.+ Umu ndi mmene Penina anali kusautsira Hana, moti Hana anali kulira ndiponso sankadya. Yesaya 66:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.
7 Chaka ndi chaka+ iye anali kuchita zimenezi nthawi zonse akapita kunyumba ya Yehova.+ Umu ndi mmene Penina anali kusautsira Hana, moti Hana anali kulira ndiponso sankadya.
23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.