Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+ Nehemiya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo anapeza kuti m’chilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose+ analembamo kuti ana a Isiraeli azikhala m’misasa+ pa nthawi ya chikondwerero m’mwezi wa 7.+ Yohane 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komabe chikondwerero cha Ayuda, chikondwerero cha misasa+ chinali pafupi.
34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+
14 Pamenepo anapeza kuti m’chilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose+ analembamo kuti ana a Isiraeli azikhala m’misasa+ pa nthawi ya chikondwerero m’mwezi wa 7.+