Levitiko 23:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Muzikhala m’misasa masiku 7.+ Mbadwa zonse za Isiraeli zizikhala m’misasa,+ Deuteronomo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa. Zekariya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+ Yohane 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komabe chikondwerero cha Ayuda, chikondwerero cha misasa+ chinali pafupi.
13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.
16 “Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse amene akubwera kudzamenyana ndi Yerusalemu,+ azidzapita kukagwadira Mfumu,+ Yehova wa makamu,+ chaka ndi chaka,+ ndi kukachita nawo chikondwerero cha misasa.+