Salimo 86:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+ Yesaya 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’tsiku limenelo kudzalira lipenga lomveka kutali.+ Ndiyeno anthu amene akuwonongeka m’dziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana m’dziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira+ Yehova m’phiri loyera ku Yerusalemu.+ Yeremiya 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Mowabu wafunkhidwa, ndipo munthu wina adzaukira mizinda yake.+ Anyamata osankhidwa a m’mizindayo apita kokaphedwa,’+ yatero Mfumu imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Aroma 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso amati: “Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu, ndipo anthu onse amutamande.”+
9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+
13 M’tsiku limenelo kudzalira lipenga lomveka kutali.+ Ndiyeno anthu amene akuwonongeka m’dziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana m’dziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira+ Yehova m’phiri loyera ku Yerusalemu.+
15 “‘Mowabu wafunkhidwa, ndipo munthu wina adzaukira mizinda yake.+ Anyamata osankhidwa a m’mizindayo apita kokaphedwa,’+ yatero Mfumu imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+