Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 43:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+

  • Hoseya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iwo anali kupereka nsembe zanyama ngati mphatso kwa ine+ ndipo anali kuzidya, koma ine Yehova sindinakondwere nazo.+ Tsopano ndidzakumbukira zolakwa zawo. Ndidzawaimba mlandu chifukwa cha machimo awo+ ndiponso chifukwa chakuti iwo anabwerera ku Iguputo.+

  • Zekariya 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzawabweretsa kuchokera kudziko la Iguputo.+ Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera ku Asuri.+ Ndidzawabweretsa kudera la Giliyadi+ ndi la Lebanoni chifukwa chakuti malo okwanira anthu onsewo sadzapezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena