Zekariya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawabweretsa kuchokera kudziko la Iguputo.Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kudziko la Asuri.+Ndidzawabweretsa kudera la Giliyadi+ ndi la Lebanoni Ndipo malo okwanira anthu onsewo sadzapezeka.+
10 Ndidzawabweretsa kuchokera kudziko la Iguputo.Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kudziko la Asuri.+Ndidzawabweretsa kudera la Giliyadi+ ndi la Lebanoni Ndipo malo okwanira anthu onsewo sadzapezeka.+