Yeremiya 50:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli ndi ku Basana.+ Ndipo iye adzakhutira mʼmapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+ Mika 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale.
19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli ndi ku Basana.+ Ndipo iye adzakhutira mʼmapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+
14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale.