Zekariya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawabweretsa kuchokera kudziko la Iguputo.+ Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera ku Asuri.+ Ndidzawabweretsa kudera la Giliyadi+ ndi la Lebanoni chifukwa chakuti malo okwanira anthu onsewo sadzapezeka.+
10 Ndidzawabweretsa kuchokera kudziko la Iguputo.+ Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera ku Asuri.+ Ndidzawabweretsa kudera la Giliyadi+ ndi la Lebanoni chifukwa chakuti malo okwanira anthu onsewo sadzapezeka.+